Skip to main content

Posts

Showing posts with the label qr code

Scanning Bar and QR codes

For a while now, we have seen how till operators from big retail shops (Chipuku or Shoprite, etc) would serve us an outstanding bill so quickly despite how many groceries we have bought. kungofika pa till, opanga uja timaona wanyamula zomwe tagula nkumazipanga scan pompo ndekuti dzina ndi price zimaonekelatu. the same thing happens ku chipatala especially central hospitals, data clerk amangotenga ka bukhu kathu koti pali zimizele nkupanga scan, ma details athu kubwelelatu pompo. zomwe ndakamba mwambamo takhala tikuziona koma anthu ambiri sitimadziwa kuti pofika masiku ano pa phone pathu pamene zimatha kutheka. Well let me break the news zikutheka ndithu, pano anthu akamagulitsana katundu, kuti adziwe ngati katundu ali wa original amangopanga scan. Koma kodi amapanga bwanji? or Mwina nanuso mukufuna phone yanu izipanga zimenezi. choyamba pali barcode. Kenako pali QR code. zithunzi zimenezi zimanyamula information yomwe opangawo adaisindikiza Kenako kuisandutsa iz...