Skip to main content

Posts

Showing posts with the label Data

Transferring everything to a new phone on Android

Why CloneIt is the Ultimate Data Migration Tool When switching Android devices, CloneIt solves these common problems: ⏳  Time-consuming  manual file transfers 📉  High risk  of missing important data 💸  No need  for expensive cloud storage 🔌  Works without  internet or cables Step-by-Step: How to Transfer Everything with CloneIt Preparation (Both Phones) Install CloneIt  from Google Play Store on both devices Charge phones  to at least 50% battery Enable WiFi  and Bluetooth on both devices Connection Process Step Sender (Old Phone) Receiver (New Phone) 1 Open CloneIt Open CloneIt 2 Tap "Send" Tap "Receive" 3 Select data types: ☑ Contacts ☑ Messages ☑ Media ☑ Apps ☑ Settings Wait for connection 4 Scan QR code or select device from list Show QR code or appear in list Advanced Transfer Options Selective transfer : Choose only what you need Compression : Faster transfers for large files Resume capability : Continue interrupted transfe...

Getting started with DHIS2 via Lenovo Tab 10

Lenovo Tab 10, imalowa simcard koma imakanika kulandila ma calls komanso imakanika kuyimbila anthu ena. Pa chifukwa ichi kulowetsa ma units kumavutilapo, koma ma SMS amafika bwino bwino. ( Pangani phone yanu isamadye maunits kwambiri ) Phone imeneyi imadalila WiFi Access point, kapena kutumizilidwa ma units, komaso internet data kuchoka pa phone ina ( kuti mudziwe zambiri zokhudza WiFi ) Njira yachidule yolowetsa ma units pa phone imeneyi kudzela TNM Ngati muli ndi simcard ya TNM, Pitani ku tsamba ili topup.tnm.co.mw/prepaid/ ndipo ndiyaulele. Choyamba mukafika pa tsamba limeneli imaonetselatu phone number yanu, balance ya ma units, current bundle status, etc. Mukaonetsetsa m'mwambamo pali "recharge". Mukapita pamenepo mupeza polemba number yanu, m'munsi mwake muli poyenela kulowetsa ma numbers omwe ali pa scratch card yanu. Kenako pansi pake pali button la green lomwe mumasindikiza mukamaliza kulowetsa ma numbers apa scratch card, ndipo ngati network ili ...