Skip to main content

Posts

Showing posts with the label airtime

Getting started with DHIS2 via Lenovo Tab 10

Lenovo Tab 10, imalowa simcard koma imakanika kulandila ma calls komanso imakanika kuyimbila anthu ena. Pa chifukwa ichi kulowetsa ma units kumavutilapo, koma ma SMS amafika bwino bwino. ( Pangani phone yanu isamadye maunits kwambiri ) Phone imeneyi imadalila WiFi Access point, kapena kutumizilidwa ma units, komaso internet data kuchoka pa phone ina ( kuti mudziwe zambiri zokhudza WiFi ) Njira yachidule yolowetsa ma units pa phone imeneyi kudzela TNM Ngati muli ndi simcard ya TNM, Pitani ku tsamba ili topup.tnm.co.mw/prepaid/  ndipo ndiyaulele. Choyamba mukafika pa tsamba limeneli imaonetselatu phone number yanu, balance ya ma units, current bundle status, etc. Mukaonetsetsa m'mwambamo pali "recharge". Mukapita pamenepo mupeza polemba number yanu, m'munsi mwake muli poyenela kulowetsa ma numbers omwe ali pa scratch card yanu. Kenako pansi pake pali button la green lomwe mumasindikiza mukamaliza kulowetsa ma numbers apa scratch card, ndipo ngati network ili...