Skip to main content

Services in Nkhotakota, Malawi.

If you are in the lakeshore district, Nkhotakota, Malawi. Well you're in luck. Palibeso zomapita kutali to get the following services;

1. Software installations. Kuika windows os, Inde windows 10, office package 365, achina VLC, antivirus, ndizamuphone zomwe ngati WhatsApp, android games etc.

2. Software activation. Timapangaso activate ma software, windows os or office asamachite kulemba "windows not genuine", zimaoneka zachibwana koma tsiku lina umangozindikila zasiya kugwila

3. Risk management, Ku office kwanu kuja kaya inuso za personal, kudzaona ma conditions a computer yanu, chifukwa penatu zimangokhala ngati kudikilila disaster yoti mutha kuipewa. We can give you recommendations.

4. Preventive maintenance. Pali zinthu zina zopeweka ndithu if you act early. Kusasa fumbi (blowing) nkati mwa computer, komaso imapezeka  computer ili very slow ngakhale space ilipo yokwana, zimafunika ife zimenezo tigwilegwilepo (disk clean up etc) isachite kufa mukuona.

5. Virus removal. Kuchotsa ma virus ndi zinthu zina for example umangozindikila file ya 1GB yasanduka 0kb. 

6. Data recovery. Ukadaulo obwezeletsa zofufutidwa.

These services are offered upon an agreement (contract) or simply a walk in, kungoimba phone basi 0992116674.


Dziwani ICT shop provides services under a registered parent business; Information Technology Services & Consultants (ITS consultants).

Comments